Ezekieli 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndinabweza dzanja langa+ ndi kuchita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa mitundu ya anthu amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.+
22 Ine ndinabweza dzanja langa+ ndi kuchita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa mitundu ya anthu amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.+