Ezekieli 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu,+ kuti ndidzawabalalitsira ku mitundu ya anthu ndi kuwamwazira m’mayiko osiyanasiyana,+
23 Komanso ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu,+ kuti ndidzawabalalitsira ku mitundu ya anthu ndi kuwamwazira m’mayiko osiyanasiyana,+