Ezekieli 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ndinawafunsa kuti, ‘Kodi malo okwezekawa ndi a chiyani? Kodi mumachitako chiyani kumeneko kuti malowo azitchedwa kuti Malo Okwezeka mpaka lero?’”’+
29 Choncho ndinawafunsa kuti, ‘Kodi malo okwezekawa ndi a chiyani? Kodi mumachitako chiyani kumeneko kuti malowo azitchedwa kuti Malo Okwezeka mpaka lero?’”’+