Ezekieli 20:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Ndithu zimene mukuganiza+ sizichitika.+ Inu mukunena kuti: “Tiyeni tikhale ngati anthu a mitundu ina. Tikhale ngati mabanja a m’mayiko ena+ potumikira mitengo ndi miyala.”’”+
32 ‘Ndithu zimene mukuganiza+ sizichitika.+ Inu mukunena kuti: “Tiyeni tikhale ngati anthu a mitundu ina. Tikhale ngati mabanja a m’mayiko ena+ potumikira mitengo ndi miyala.”’”+