Ezekieli 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 ‘Ndidzakudutsitsani pansi pa ndodo ya m’busa+ ndi kuchita nanu pangano lolimba.+