Ezekieli 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anakupanga ndi matabwa a mtengo wa mlombwa okhaokha ochokera ku Seniri.+ Anatenga mkungudza wa ku Lebanoni+ kuti ukhale mtengo wako womangirirapo chinsalu choyendetsera ngalawa.
5 Anakupanga ndi matabwa a mtengo wa mlombwa okhaokha ochokera ku Seniri.+ Anatenga mkungudza wa ku Lebanoni+ kuti ukhale mtengo wako womangirirapo chinsalu choyendetsera ngalawa.