Ezekieli 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Unalemba ntchito Aluya+ ndi atsogoleri onse a ku Kedara+ kuti azikugulitsira malonda. Iwo anali kukugulitsira ana a nkhosa amphongo, nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+
21 Unalemba ntchito Aluya+ ndi atsogoleri onse a ku Kedara+ kuti azikugulitsira malonda. Iwo anali kukugulitsira ana a nkhosa amphongo, nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+