Ezekieli 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzakukola ndi ngowe munsagwada zako+ ndi kuchititsa nsomba za m’ngalande za mtsinje wa Nailo kukakamira kumamba ako. Ndidzakutulutsa m’ngalande za Nailo pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalandezo zimene zakakamira kumamba ako.
4 Ndidzakukola ndi ngowe munsagwada zako+ ndi kuchititsa nsomba za m’ngalande za mtsinje wa Nailo kukakamira kumamba ako. Ndidzakutulutsa m’ngalande za Nailo pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalandezo zimene zakakamira kumamba ako.