Ezekieli 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’dziko lako simudzaponda phazi la munthu+ kapena la chiweto,+ ndipo simudzakhala munthu aliyense kwa zaka 40.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:11 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 8
11 M’dziko lako simudzaponda phazi la munthu+ kapena la chiweto,+ ndipo simudzakhala munthu aliyense kwa zaka 40.+