Ezekieli 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Zaka 40 zikadzatha,+ ndidzasonkhanitsa pamodzi Aiguputowo kuchokera pakati pa anthu a mitundu ina kumene adzabalalikire.+
13 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Zaka 40 zikadzatha,+ ndidzasonkhanitsa pamodzi Aiguputowo kuchokera pakati pa anthu a mitundu ina kumene adzabalalikire.+