Ezekieli 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ufumu wawo udzakhala wotsika kusiyana ndi maufumu ena ndipo sudzadzikwezanso pamaso pa mitundu ina ya anthu.+ Ndidzawachepetsa kwambiri moti sadzakhalanso ndi mphamvu zolamulira mitundu ina ya anthu.+
15 Ufumu wawo udzakhala wotsika kusiyana ndi maufumu ena ndipo sudzadzikwezanso pamaso pa mitundu ina ya anthu.+ Ndidzawachepetsa kwambiri moti sadzakhalanso ndi mphamvu zolamulira mitundu ina ya anthu.+