Ezekieli 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba ya Isiraeli sidzawadaliranso.+ Aisiraeli sadzachititsa kuti zolakwa zawo zikumbukiridwe mwa kutembenukira kwa Iguputo,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’”
16 Nyumba ya Isiraeli sidzawadaliranso.+ Aisiraeli sadzachititsa kuti zolakwa zawo zikumbukiridwe mwa kutembenukira kwa Iguputo,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’”