Ezekieli 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Pa tsikulo, ndidzaphukitsira nyumba ya Isiraeli nyanga.*+ Iwe ndidzakupatsa mpata kuti utsegule pakamwa pako pakati pawo,+ ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”
21 “Pa tsikulo, ndidzaphukitsira nyumba ya Isiraeli nyanga.*+ Iwe ndidzakupatsa mpata kuti utsegule pakamwa pako pakati pawo,+ ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”