Ezekieli 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzatsanulira mkwiyo wanga+ pa Sini, malo otetezedwa kwambiri a Iguputo, ndipo ndidzapha khamu la anthu a ku No.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:15 Nsanja ya Olonda,7/1/2003, tsa. 32
15 Ndidzatsanulira mkwiyo wanga+ pa Sini, malo otetezedwa kwambiri a Iguputo, ndipo ndidzapha khamu la anthu a ku No.+