Ezekieli 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzapereka ziweruzo mu Iguputo+ ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”