Ezekieli 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndithana ndi Farao mfumu ya Iguputo.+ Ndidzathyola manja ake onse,+ dzanja lamphamvu ndi lothyoka lija,+ ndipo ndidzachititsa kuti lupanga ligwe m’dzanja lake.+
22 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndithana ndi Farao mfumu ya Iguputo.+ Ndidzathyola manja ake onse,+ dzanja lamphamvu ndi lothyoka lija,+ ndipo ndidzachititsa kuti lupanga ligwe m’dzanja lake.+