Ezekieli 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzalimbitsa manja a mfumu ya Babulo ndipo Farao adzagwetsa manja ake. Ndikadzapereka lupanga langa m’manja mwa mfumu ya Babulo, iye n’kuligwiritsa ntchito pomenyana ndi dziko la Iguputo, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
25 Ndidzalimbitsa manja a mfumu ya Babulo ndipo Farao adzagwetsa manja ake. Ndikadzapereka lupanga langa m’manja mwa mfumu ya Babulo, iye n’kuligwiritsa ntchito pomenyana ndi dziko la Iguputo, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+