Ezekieli 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtengowo unakula kwambiri chifukwa cha madzi.+ Unatalika chifukwa cha madzi akuya. Madziwo anali kuyenda m’mitsinje kuzungulira pamalo pamene mtengowo unabzalidwa. Ngalande za madziwo zinakafika kumitengo yonse ya kumeneko.
4 Mtengowo unakula kwambiri chifukwa cha madzi.+ Unatalika chifukwa cha madzi akuya. Madziwo anali kuyenda m’mitsinje kuzungulira pamalo pamene mtengowo unabzalidwa. Ngalande za madziwo zinakafika kumitengo yonse ya kumeneko.