Ezekieli 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chake mtengowo unatalika kwambiri kuposa mitengo yonse yakumaloko.+ “‘Nthambi zake zikuluzikulu zinali kuchuluka, ndipo nthambi zina zinapitiriza kutalika chifukwa cha kuchuluka kwa madzi m’ngalande zake.+
5 N’chifukwa chake mtengowo unatalika kwambiri kuposa mitengo yonse yakumaloko.+ “‘Nthambi zake zikuluzikulu zinali kuchuluka, ndipo nthambi zina zinapitiriza kutalika chifukwa cha kuchuluka kwa madzi m’ngalande zake.+