Ezekieli 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mtengowo unakongola kwambiri+ chifukwa cha kukula kwake ndi kutalika kwa nthambi zake zamasamba ambiri. Izi zinachitika chifukwa chakuti mizu yake inali pamadzi ambiri.
7 Mtengowo unakongola kwambiri+ chifukwa cha kukula kwake ndi kutalika kwa nthambi zake zamasamba ambiri. Izi zinachitika chifukwa chakuti mizu yake inali pamadzi ambiri.