Ezekieli 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zidzakhala pathunthu lake logwetsedwalo, ndipo nyama zonse zakutchire zidzakhala m’nthambi zake.+
13 Zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zidzakhala pathunthu lake logwetsedwalo, ndipo nyama zonse zakutchire zidzakhala m’nthambi zake.+