-
Ezekieli 31:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsiku limene mtengo wamkungudza udzatsikire ku Manda* ndidzachititsa anthu kulira.+ Ndidzaphimba madzi akuya chifukwa cha mtengowo. Ndidzachita izi kuti ndiimitse madzi m’mitsinje yake ndi kutseka madzi ambiri. Ndidzachititsa mdima mu Lebanoni chifukwa cha mtengowo ndipo mitengo yonse yakutchire idzafota.
-