Ezekieli 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mitengo imeneyi yatsikira ku Manda pamodzi ndi mtengo wa mkungudzawo.+ Yatsikira kwa ophedwa ndi lupanga ndi kwa amene ankakhala mumthunzi wake pakati pa mitundu ina ya anthu monga mbewu yake.’+
17 Mitengo imeneyi yatsikira ku Manda pamodzi ndi mtengo wa mkungudzawo.+ Yatsikira kwa ophedwa ndi lupanga ndi kwa amene ankakhala mumthunzi wake pakati pa mitundu ina ya anthu monga mbewu yake.’+