Ezekieli 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzachititsa dziko kumwa zinthu zotuluka m’thupi mwako. Ndidzalichititsa kumwa magazi+ ako m’mapiri. Mitsinje idzadzaza ndi zinthu zotuluka m’thupi mwako.’
6 Ndidzachititsa dziko kumwa zinthu zotuluka m’thupi mwako. Ndidzalichititsa kumwa magazi+ ako m’mapiri. Mitsinje idzadzaza ndi zinthu zotuluka m’thupi mwako.’