-
Ezekieli 32:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 “‘Pa nthawi imeneyo ndidzayeretsa madzi awo, ndipo madzi a m’mitsinje yawo adzayenda ngati mafuta,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
-