Ezekieli 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Ndikadzasandutsa dziko la Iguputo bwinja ndipo zinthu zonse za m’dzikolo zikadzawonongedwa,+ komanso ndikadzapha anthu onse okhala m’dzikolo, anthu a mitundu ina adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
15 “‘Ndikadzasandutsa dziko la Iguputo bwinja ndipo zinthu zonse za m’dzikolo zikadzawonongedwa,+ komanso ndikadzapha anthu onse okhala m’dzikolo, anthu a mitundu ina adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+