Ezekieli 32:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Imeneyi ndi nyimbo yoimba polira ndipo anthu adzaiimba. Ana aakazi a mitundu ina ya anthu adzaiimba. Nyimbo imeneyi adzaimbira Iguputo ndi khamu lake lonse,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
16 “‘Imeneyi ndi nyimbo yoimba polira ndipo anthu adzaiimba. Ana aakazi a mitundu ina ya anthu adzaiimba. Nyimbo imeneyi adzaimbira Iguputo ndi khamu lake lonse,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”