Ezekieli 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Aiguputo adzaphedwa pamodzi ndi anthu ophedwa ndi lupanga.+ Dzikolo laperekedwa ku lupanga. Anthu inu, kokerani kutali dzikolo ndi khamu lake lonse.
20 “‘Aiguputo adzaphedwa pamodzi ndi anthu ophedwa ndi lupanga.+ Dzikolo laperekedwa ku lupanga. Anthu inu, kokerani kutali dzikolo ndi khamu lake lonse.