Ezekieli 35:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uuze deralo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe dera lamapiri la Seiri,+ ine ndithana nawe. Nditambasula dzanja langa ndi kukukhaulitsa.+ Ndikusandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka.+
3 Uuze deralo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe dera lamapiri la Seiri,+ ine ndithana nawe. Nditambasula dzanja langa ndi kukukhaulitsa.+ Ndikusandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka.+