Ezekieli 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 chifukwa chakuti unali ndi chidani chosatha+ ndi ana a Isiraeli ndipo unali kuwapha ndi lupanga.+ Unachita zimenezi pa nthawi ya tsoka lawo,+ pamene zolakwa zawo zinafika kumapeto.”’+
5 chifukwa chakuti unali ndi chidani chosatha+ ndi ana a Isiraeli ndipo unali kuwapha ndi lupanga.+ Unachita zimenezi pa nthawi ya tsoka lawo,+ pamene zolakwa zawo zinafika kumapeto.”’+