Ezekieli 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dera lamapiri la Seiri ndidzalisandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka.+ Kumeneko sikudzapezeka aliyense wodutsako.+
7 Dera lamapiri la Seiri ndidzalisandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka.+ Kumeneko sikudzapezeka aliyense wodutsako.+