Ezekieli 35:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’mapirimo ndidzadzazamo anthu ophedwa. M’zitunda zako, m’zigwa zako ndi m’mitsinje yako yonse, mudzadzaza anthu ophedwa ndi lupanga.+
8 M’mapirimo ndidzadzazamo anthu ophedwa. M’zitunda zako, m’zigwa zako ndi m’mitsinje yako yonse, mudzadzaza anthu ophedwa ndi lupanga.+