Ezekieli 35:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakusandutsa malo omwe adzakhale owonongeka mpaka kalekale. M’mizinda yako simudzakhalanso anthu,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:9 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 24
9 Ndidzakusandutsa malo omwe adzakhale owonongeka mpaka kalekale. M’mizinda yako simudzakhalanso anthu,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+