Ezekieli 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Chotero pali ine Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘Ndidzachitapo kanthu mogwirizana ndi mkwiyo wako ndi nsanje imene unaisonyeza chifukwa chakuti unali kudana nawo,+ ndipo ndikadzakuweruza, iwo adzandidziwa.+
11 ‘Chotero pali ine Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘Ndidzachitapo kanthu mogwirizana ndi mkwiyo wako ndi nsanje imene unaisonyeza chifukwa chakuti unali kudana nawo,+ ndipo ndikadzakuweruza, iwo adzandidziwa.+