Ezekieli 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma inu mapiri a Isiraeli, mudzatulutsa nthambi ndi kubalira zipatso anthu anga Aisiraeli,+ chifukwa chakuti atsala pang’ono kulowa m’dziko lino.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:8 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 24
8 Koma inu mapiri a Isiraeli, mudzatulutsa nthambi ndi kubalira zipatso anthu anga Aisiraeli,+ chifukwa chakuti atsala pang’ono kulowa m’dziko lino.+