Ezekieli 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo ndinawatsanulira mkwiyo wanga chifukwa cha magazi amene iwo anakhetsa m’dziko+ limenenso analidetsa ndi mafano awo onyansa.+
18 Pamenepo ndinawatsanulira mkwiyo wanga chifukwa cha magazi amene iwo anakhetsa m’dziko+ limenenso analidetsa ndi mafano awo onyansa.+