Ezekieli 36:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu a mitundu ina okuzungulirani amene adzatsale, adzadziwa kuti ine Yehova, ndamanga zinthu zimene zinagwetsedwa.+ Adzadziwa kuti ndabzala mitengo m’dziko limene linali bwinja. Ine Yehova ndanena zimenezi ndipo ndazichita.’+
36 Anthu a mitundu ina okuzungulirani amene adzatsale, adzadziwa kuti ine Yehova, ndamanga zinthu zimene zinagwetsedwa.+ Adzadziwa kuti ndabzala mitengo m’dziko limene linali bwinja. Ine Yehova ndanena zimenezi ndipo ndazichita.’+