Ezekieli 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsikulo maganizo adzakubwerera mumtima mwako+ ndipo udzaganiza zochita chiwembu choipa kwambiri.+
10 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsikulo maganizo adzakubwerera mumtima mwako+ ndipo udzaganiza zochita chiwembu choipa kwambiri.+