Ezekieli 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Kodi iwe ndiwe+ yemwe uja amene ndinkakunena kale kudzera mwa atumiki anga, aneneri a Isiraeli? Aneneriwo ankalosera chaka ndi chaka m’masiku amenewo kuti ndidzakutumiza kwa iwo kuti ukawaukire.’+
17 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Kodi iwe ndiwe+ yemwe uja amene ndinkakunena kale kudzera mwa atumiki anga, aneneri a Isiraeli? Aneneriwo ankalosera chaka ndi chaka m’masiku amenewo kuti ndidzakutumiza kwa iwo kuti ukawaukire.’+