Ezekieli 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ananditengera kumeneko ndipo ndinaonako munthu wamwamuna. Munthuyo anali kuoneka wonyezimira ngati mkuwa.+ M’manja mwake munali chingwe cha fulakesi* ndi bango loyezera,+ ndipo anaima pachipata. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2150, 2241 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 103/1/1999, ptsa. 9, 14
3 Kenako ananditengera kumeneko ndipo ndinaonako munthu wamwamuna. Munthuyo anali kuoneka wonyezimira ngati mkuwa.+ M’manja mwake munali chingwe cha fulakesi* ndi bango loyezera,+ ndipo anaima pachipata.
40:3 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2150, 2241 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 103/1/1999, ptsa. 9, 14