-
Ezekieli 40:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kenako anayeza m’lifupi mwa malo apafupi ndi khomo la kanyumba ka pachipata n’kupeza mikono 10. Anayezanso m’litali mwa chipata n’kupeza mikono 13.
-