-
Ezekieli 40:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kanyumba ka pachipata kameneka ndi khonde lake zinali ndi mawindo ofanana ndi a tinyumba ta zipata zina zija kuzungulira kanyumbako. M’litali, kanyumbako kanali mikono 50 ndipo m’lifupi kanali mikono 25.
-