-
Ezekieli 40:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Tinyumba tonse ta zipata zolowera m’bwalo lamkati tinali ndi khonde. M’litali mwake khondelo linali mikono 25 ndipo m’lifupi linali mikono isanu.
-