Ezekieli 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Khonde lake linayang’ana kubwalo lakunja. Pazipilala zake zam’mbali panali zithunzi za mtengo wa kanjedza+ ndipo masitepe olowera m’kanyumba ka pachipatako analipo 8.+
31 Khonde lake linayang’ana kubwalo lakunja. Pazipilala zake zam’mbali panali zithunzi za mtengo wa kanjedza+ ndipo masitepe olowera m’kanyumba ka pachipatako analipo 8.+