-
Ezekieli 40:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Iye anayeza zipinda za alonda, zipilala zake zam’mbali ndi khonde lake. Kanyumba ka pachipata konseko kanali ndi mawindo. M’litali mwake, kanyumba kameneka kanali mikono 50 ndipo m’lifupi mwake kanali mikono 25.
-