Ezekieli 40:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zipilala zake zam’mbali zinayang’ana kubwalo lakunja. Pazipilala zam’mbalizo panali zithunzi za mtengo wa kanjedza kumbali iyi ndi kumbali inayo.+ Masitepe olowera m’kanyumba ka pachipatako analipo 8.
37 Zipilala zake zam’mbali zinayang’ana kubwalo lakunja. Pazipilala zam’mbalizo panali zithunzi za mtengo wa kanjedza kumbali iyi ndi kumbali inayo.+ Masitepe olowera m’kanyumba ka pachipatako analipo 8.