Ezekieli 40:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pafupi ndi zipilala zam’mbali mwa tinyumba ta zipatazo panali chipinda chodyeramo. Kumeneko n’kumene anali kutsukira nsembe yopsereza yathunthu.+
38 Pafupi ndi zipilala zam’mbali mwa tinyumba ta zipatazo panali chipinda chodyeramo. Kumeneko n’kumene anali kutsukira nsembe yopsereza yathunthu.+