-
Ezekieli 40:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Kunja kwa kanyumba ka pachipatako kunali matebulo anayi ndipo mkati mwa kanyumbako munalinso matebulo anayi. Matebulo onse amene anali kupherapo nyama analipo 8.
-