Ezekieli 40:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Khonde la nyumbayo linali mikono 20 m’litali mwake ndi mikono 11 m’lifupi. Kuti munthu afike pakhondepo anali kukwera masitepe. Pafupi ndi zipilala zam’mbalizo panali nsanamira, imodzi mbali iyi, ina mbali inayo.+
49 Khonde la nyumbayo linali mikono 20 m’litali mwake ndi mikono 11 m’lifupi. Kuti munthu afike pakhondepo anali kukwera masitepe. Pafupi ndi zipilala zam’mbalizo panali nsanamira, imodzi mbali iyi, ina mbali inayo.+