-
Ezekieli 41:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Khomo lolowera m’chipinda chakunja linali lalikulu mikono 10, ndipo kuchokera pakhomolo kukafika pakona panali khoma la mikono isanu mbali iyi, ndi mikono isanu mbali inayo. Anayezanso m’litali mwa chipinda chakunja ndipo chinali mikono 40, m’lifupi mwake chinali mikono 20.
-